KUFOTOKOZA MOMWE ANTHU ENA AMAYANKHULIRA AKAPITA MAYIKO AKUNJA KWA ZIKO LAWO KUKAGWIRA NTCHITO. IWO AMATI, TINABWELERA NTCHITO KUNO OSATI KUPEMPHERA, TIZAKAPANGA ZACHIPEMBEZO TIKAZABWELERA KUPITA KUMUZI KWATHU. MUNO NDI MOYENDA.